
Nduna yoona za zofalitsa nkhani, Shadric Namalomba yatsindika kufunika koti mabungwe a boma azigwirizana pa ntchito pa ulendo wawo ku likulu la MACRA ku Chichiri, Blantyre.
Mkulu wa MACRA, a Mayamiko Nkoloma, anathokoza ulendowu.
#macra
#DigitallyTransformedMalawi
#261TollFree




































