jorge ochoa
4.1K posts

jorge ochoa
@justdenn12
ICT Officer/Farmer/Father/Husband /Son/Brother/Friend/Foe Ecclesiastes 3 :1
Malawi Katılım Ekim 2018
782 Takip Edilen778 Takipçiler

@DemobreyPilDash They look out for eachother, petroda ndiya amwenye amasungilana.
English
jorge ochoa retweetledi

@EricFarai Account imakhala ya bwana, pa counter barman amangopanga record trans id, it is verified nthawi yopanga stock which will be the following day.
Filipino

Fake transactions. Why are they always caught at a bar?
hiiii kaya@its_stv
MUBAS (FORMERLY POLYTECHNIC) STUDENTS CAUGHT STEALING Student wa ku MUBAS dzulo amugwira pa Kudya pa pub ya a Philly. Iyeyo amamwa mowa kenaka kumatumiza ma text (omwe amafika ngati ma SMS) pretending ngati akuchokera ku Mo626.
English

@justdenn12 Nde kusintha ownership buyer azizati "koma galimoto yanu ija mpaka 120mil", iwe "chani!?"😂😂😂😂 I think just to even the pain you just say ine ndimafuna 60tu 😂 😂😂😂
Indonesia

@DZimatron22 In these type of deals agent amayesesa buyer asamuziwe mwini galimoto, muzakumana kokasintha ownership
Indonesia

@justdenn12 Koma mesa pokawona galimoto some may meet with the owner but I guess in most cases agent amakhala in the forefront of everything nde akudye kuwili koma ana adyelekezi won't see heaven 😂😂😂😂😂
English

@Nate2V How can you let it mpaka getting that big opanda kukalandila thandizo ku hospa? Kapena nthenda imeneyi nawo njpanda khini
Indonesia

This not a benign tumor, hydrocele iyi caused by microfilaria.
【厳選】マジで怖い動画@kowa_maji222
様々な事情により、●丸にできた良性腫瘍を何年も治療せずに過ごした男性は、まるで象の●丸のような状態で生活せざるを得なかった。
English

@tiidrotafrikka2 Uwu ndi muvi wachiponyeponye abro, kupanda kusamala umakulasa utangozikhalila pheee
Indonesia

@MakileniMadalo Asiyeni, tizitchelabe happy hour ku DAPP ife 🤣🤣🤣
Filipino

@GennaGenna265 @Kamoza0104 Ku banja nkosekesa amwene 🤣🤣🤣 umamukwiila munthu oti ukugona naye pambalipa daily. Akachedwa kubwela kogona iwe mkumabowekaso kut kodi akuchedwa kut ameneyu. Akafika ukupinda mlomo kut uzioneka wakwiya 🤣🤣🤣
Indonesia

@justdenn12 @Kamoza0104 My aunt once told me akanafuna bw3z atasiyana kalekale mpamene i understood uona akuzuka omwewo at 4 kuika madzi osamba pamoto biggy isambe kukonza breakfast 😂😂..
Ku banja kuli secret yoti not a lot of us understand we are quick to judge
Filipino

@MrRamGee @Kamoza0104 Generaly women run away from accountability. They are good at playing victim
English

@FridahMagedi Pa ulemu wake olo ukuziwa kut olakwa ndi uyu mwana sakhalisa pansi makolo ake. the best you can do ndikupeza wachibale wamkulu or mzawo wa makolowo ndikumupempha kut akhale nawo pansi and resolve their issues
Indonesia

@justdenn12 Sititenga mbali when you don't know olakwatu koma uchita kudziwa olakwa,why not take a side
Indonesia

@mjcatie Akulu mwadya 1 pamudzi pano. Pangani zoti ma twitter inlaws tikamwe fanta 🤣🤣🤣🤣
Indonesia




















