Sabitlenmiş Tweet
Wikise1992
7.4K posts

Wikise1992
@Wikise1
Wikise1992 is a Malawian popular Musician & Multi Award winning Artist. #GHETTO_ENTERTAINERS👌
Malawi Katılım Aralık 2018
372 Takip Edilen34.6K Takipçiler
Wikise1992 retweetledi

So a lot of malawians don't know SHABARAKATALI song yinali beat ya #Litty by Meek mill feat Tory Lanez?🤔ine ndinkati mukudziwa tu
4peat💙🇲🇼🇿🇲@EnockChipula
@Pemphs1 @Wikise1 Koma ineyo how come i'm only hearing this now? 😂😂
Filipino

@Wikise1 🤣🤣🤣🤣 komaditu asamakunyoze coz enaso amakonda nyimbo zako
Indonesia

So ukamakhalira kunyoza music yanga nkhani yake ndi nsanje cholinga ndi fooke ndizisiye, ndizigona njala ? Mwana opusa kwambiri 😏
SNNOGHA🔝@Madala_snnogah
I don't remember the person but someone tweeted about Shipmark kut Shipmark alibe luso content creation angosiya that was 2 moth ago I think, so I just wanted to say kut Pali anthu ena amayankhula mopusa zamzawo cholinga mufooke kma osafooka magaye, alot of people like him now
Indonesia

@Wikise1 @Laflemokaris 😭😂😂😂😂ngat amakhala kwao bwanji?
Indonesia

Inu nayamba kumvela Drake muma 2009 nde mukati ndife tomwe nde kuti chani ? Kodi mukamationa tuyimba za lokolo basi mumaona ngati nde life yathu? We do it for business and i understand music industry ya kwathu kuno, otherwise ine ndi Team Drizzy since young money days🫰
𝒾𝐃 🌟@crynocte
💀😂koma Ku malawi nkonkoma. Ndi wikise yemwe Drake😂💀
Filipino

@EnockChipula @Pemphs1 Coz of style yamayimbidwe yinali ya chilendo and yinali ya comedy nde munali busy nkuseka 😂
Filipino

@Wikise1 your top fan Snoggah is behind that account bro😂😂he thought we wont know
English

@Wikise1 @EKamponda68602 Akuona ngt basi poto umayimba local ndekut umangovela achina Mbenjele basi 😂
Indonesia

@Pemphs1 Ambiridi sadziwa ndithu kuti beat ya Shabarakatali ndiya meek mill litty feat Tory lanez😂😂 akuona ngati timangomvera achina gwaladi
Indonesia

@Wikise1 Awuze kuti unakwela chi beat Cha Litty Again and made a hit out of it...ambili samadsiwa 😂😂
Filipino

@Laflemokaris Ana achibwana kwambiri mpaka gate keeping kumvela Drake ko 😂😂 nthawi yomwe tinayamba kumvela Drake iwowo akukowa dongo 😂
Indonesia












